Levitiko 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzisunga masabata anga+ ndi kuopa malo anga opatulika. Ine ndine Yehova.