Levitiko 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Pa masiku onse amene dzikolo lidzakhala bwinja, lidzabweza masabata ake, inu muli m’dziko la adani anu. Nthawi imeneyo, dziko lidzasunga sabata ndipo lidzabweza masabata ake.+
34 “‘Pa masiku onse amene dzikolo lidzakhala bwinja, lidzabweza masabata ake, inu muli m’dziko la adani anu. Nthawi imeneyo, dziko lidzasunga sabata ndipo lidzabweza masabata ake.+