Levitiko 26:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndipo ndidzakumbukira m’malo mwawo pangano limene ndinachita ndi makolo awo,+ amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo, anthu a mitundu ina akuona.+ Ndidzachita zimenezi kuti ndiwasonyeze kuti ndine Mulungu wawo. Ine ndine Yehova.’”
45 Ndipo ndidzakumbukira m’malo mwawo pangano limene ndinachita ndi makolo awo,+ amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo, anthu a mitundu ina akuona.+ Ndidzachita zimenezi kuti ndiwasonyeze kuti ndine Mulungu wawo. Ine ndine Yehova.’”