Numeri 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero Mose anawerenga anthuwo+ m’chipululu cha Sinai, monga mmene Yehova anamulamulira.