Numeri 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 “A fuko la Levi okha usawalembe mayina, ndipo usawawerengere pamodzi ndi ana a Isiraeli enawo.+