Numeri 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 “Ana a Isiraeli azimanga mahema awo, aliyense malinga ndi msasa wawo, munthu aliyense malinga ndi gulu lake la mafuko atatu,+ malinga ndi magulu awo a asilikali.
52 “Ana a Isiraeli azimanga mahema awo, aliyense malinga ndi msasa wawo, munthu aliyense malinga ndi gulu lake la mafuko atatu,+ malinga ndi magulu awo a asilikali.