Numeri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Chigawo cha mafuko atatu cha Yuda ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mawa kotulukira dzuwa. Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.
3 “Chigawo cha mafuko atatu cha Yuda ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mawa kotulukira dzuwa. Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.