Numeri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mwera. Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.
10 “Chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mwera. Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.