Numeri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chigawo cha mafuko atatu cha Efuraimu+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumadzulo. Mtsogoleri wa ana a Efuraimu ndi Elisama,+ mwana wa Amihudi.
18 “Chigawo cha mafuko atatu cha Efuraimu+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumadzulo. Mtsogoleri wa ana a Efuraimu ndi Elisama,+ mwana wa Amihudi.