Numeri 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose.+ Dongosolo limene analitsatira pomanga misasa yawo m’zigawo za mafuko atatu,+ n’limenenso anatsatira posamuka,+ aliyense m’banja lake malinga ndi nyumba ya makolo ake.
34 Ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose.+ Dongosolo limene analitsatira pomanga misasa yawo m’zigawo za mafuko atatu,+ n’limenenso anatsatira posamuka,+ aliyense m’banja lake malinga ndi nyumba ya makolo ake.