Numeri 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwo aziyala nsalu yabuluu patebulo+ la mkate wachionetsero, n’kuikapo mbale,+ zikho, mbale zolowa,+ ndi mitsuko ya nsembe yachakumwa. Mkate wachionetsero womwe ndi nsembe ya nthawi zonse+ uzikhalabe pomwepo.
7 “Iwo aziyala nsalu yabuluu patebulo+ la mkate wachionetsero, n’kuikapo mbale,+ zikho, mbale zolowa,+ ndi mitsuko ya nsembe yachakumwa. Mkate wachionetsero womwe ndi nsembe ya nthawi zonse+ uzikhalabe pomwepo.