Numeri 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akatero, aziziphimba ndi nsalu yowomba ndi ulusi wofiira kwambiri,+ ndiponso aziphimba tebulolo ndi zikopa za akatumbu.+ Kenako azibwezeretsa mitengo yake yonyamulira.+
8 Akatero, aziziphimba ndi nsalu yowomba ndi ulusi wofiira kwambiri,+ ndiponso aziphimba tebulolo ndi zikopa za akatumbu.+ Kenako azibwezeretsa mitengo yake yonyamulira.+