Numeri 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako, aziphimba guwa lansembe+ lagolide ndi nsalu yabuluu. Aziliphimbanso ndi zikopa za akatumbu,+ n’kubwezeretsa mitengo yake yonyamulira.+
11 Kenako, aziphimba guwa lansembe+ lagolide ndi nsalu yabuluu. Aziliphimbanso ndi zikopa za akatumbu,+ n’kubwezeretsa mitengo yake yonyamulira.+