Numeri 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Eleazara mwana wa wansembe Aroni, aziyang’anira+ mafuta+ a nyale, zofukiza zonunkhira,+ nsembe yanthawi zonse yambewu,+ ndi mafuta odzozera.+ Aziyang’aniranso chihema chonse chopatulika ndi zonse za mmenemo, ndiwo malo oyerawo ndi ziwiya zake.”
16 “Eleazara mwana wa wansembe Aroni, aziyang’anira+ mafuta+ a nyale, zofukiza zonunkhira,+ nsembe yanthawi zonse yambewu,+ ndi mafuta odzozera.+ Aziyang’aniranso chihema chonse chopatulika ndi zonse za mmenemo, ndiwo malo oyerawo ndi ziwiya zake.”