Numeri 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuti iwo asaphedwe poyandikira zinthu zopatulika koposa,+ koma akhalebe ndi moyo, Aroni ndi ana ake azilowa m’chihemacho. Mmenemo azigawira aliyense wa iwo ntchito ndi katundu woti anyamule.
19 Kuti iwo asaphedwe poyandikira zinthu zopatulika koposa,+ koma akhalebe ndi moyo, Aroni ndi ana ake azilowa m’chihemacho. Mmenemo azigawira aliyense wa iwo ntchito ndi katundu woti anyamule.