Numeri 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Azinyamula nsalu za chihema chopatulika+ ndi chihema chokumanako,+ ndiponso chophimba chake,+ chophimba cha chikopa cha katumbu+ chomwe chili pamwamba pake, ndi nsalu yotchinga+ pakhomo la chihema chokumanako.
25 Azinyamula nsalu za chihema chopatulika+ ndi chihema chokumanako,+ ndiponso chophimba chake,+ chophimba cha chikopa cha katumbu+ chomwe chili pamwamba pake, ndi nsalu yotchinga+ pakhomo la chihema chokumanako.