Numeri 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana a Gerisoni+ azichita utumiki wawo wonse molangizidwa ndi Aroni ndi ana ake.+ Aziwauza ntchito zimene azigwira ndi katundu amene azinyamula. Onse muziwagawira katundu amene azinyamula monga gawo lawo.
27 Ana a Gerisoni+ azichita utumiki wawo wonse molangizidwa ndi Aroni ndi ana ake.+ Aziwauza ntchito zimene azigwira ndi katundu amene azinyamula. Onse muziwagawira katundu amene azinyamula monga gawo lawo.