Numeri 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Uwu ndiwo utumiki wa mabanja a ana a Merari,+ monga gawo la utumiki wawo m’chihema chokumanako. Itamara mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo.”+
33 Uwu ndiwo utumiki wa mabanja a ana a Merari,+ monga gawo la utumiki wawo m’chihema chokumanako. Itamara mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo.”+