Numeri 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano Mose ndi Aroni, pamodzi ndi atsogoleri a anthuwo,+ anawerenga ana a Kohati+ malinga ndi mabanja awo, potsata nyumba za makolo awo.
34 Tsopano Mose ndi Aroni, pamodzi ndi atsogoleri a anthuwo,+ anawerenga ana a Kohati+ malinga ndi mabanja awo, potsata nyumba za makolo awo.