Numeri 4:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Pomvera mawu a Yehova, Mose anawawerenga, aliyense malinga ndi utumiki wake ndi katundu wake wonyamula. Anawerengedwa monga mmene Yehova analamulira Mose.+
49 Pomvera mawu a Yehova, Mose anawawerenga, aliyense malinga ndi utumiki wake ndi katundu wake wonyamula. Anawerengedwa monga mmene Yehova analamulira Mose.+