Numeri 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Wansembeyo azitenga mkaziyo n’kumuimiritsa pamaso pa Yehova.+