Numeri 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Mose anamva anthu akulira m’mabanja mwawo, munthu aliyense pakhomo la hema wake. Pamenepo mkwiyo wa Yehova unawayakira koopsa anthuwo.+ Mose nayenso anaipidwa nazo zimenezo.+
10 Tsopano Mose anamva anthu akulira m’mabanja mwawo, munthu aliyense pakhomo la hema wake. Pamenepo mkwiyo wa Yehova unawayakira koopsa anthuwo.+ Mose nayenso anaipidwa nazo zimenezo.+