-
Numeri 11:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiitenga kuti nyama yoti ndipatse anthu onsewa? Pakuti iwo akupitirizabe kundilirira ine, kuti, ‘Tipatse nyama yoti tidye!’
-