Numeri 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose anatumiza amunawo kuchokera kuchipululu cha Parana,+ monga mmene Yehova analamulira. Amuna onsewo anali atsogoleri a ana a Isiraeli.
3 Chotero Mose anatumiza amunawo kuchokera kuchipululu cha Parana,+ monga mmene Yehova analamulira. Amuna onsewo anali atsogoleri a ana a Isiraeli.