-
Numeri 13:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mukaone ngati dziko limene akukhalamo lili labwino kapena loipa, ndiponso ngati akukhala m’misasa kapena m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.
-