Numeri 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komanso mukaone ngati dzikolo lili lachonde kapena lopanda chonde,+ ngati lili ndi mitengo kapena ayi. Mukalimbe mtima+ n’kutengako zipatso za m’dzikomo.” Amenewa anali masiku amene mphesa zoyamba zinali kupsa.+
20 Komanso mukaone ngati dzikolo lili lachonde kapena lopanda chonde,+ ngati lili ndi mitengo kapena ayi. Mukalimbe mtima+ n’kutengako zipatso za m’dzikomo.” Amenewa anali masiku amene mphesa zoyamba zinali kupsa.+