-
Numeri 14:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Iwo akamva adzauza anthu a m’dziko lino, amene amva kuti inu Yehova muli pakati pa anthu anu,+ ndi kuti mumaonekera kwa iwo pamasom’pamaso.+ Inu ndinu Yehova, ndipo mtambo wanu uli pamwamba pawo. Masana mumawatsogolera mumtambo woima njo ngati chipilala, pamene usiku mumawatsogolera m’lawi lamoto.+
-