Numeri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Kora+ mwana wa Izara,+ mwana wa Kohati,+ mwana wa Levi,+ anagwirizana ndi adzukulu a Rubeni,+ omwe ndi Datani+ ndi Abiramu+ ana a Eliyabu,+ komanso Oni mwana wa Pelete, kuti aukire. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:1 Nsanja ya Olonda,8/1/2000, tsa. 10
16 Tsopano Kora+ mwana wa Izara,+ mwana wa Kohati,+ mwana wa Levi,+ anagwirizana ndi adzukulu a Rubeni,+ omwe ndi Datani+ ndi Abiramu+ ana a Eliyabu,+ komanso Oni mwana wa Pelete, kuti aukire.