Numeri 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iwo anasonkhana n’kuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni, kuti: “Tatopa nanu tsopano! Khamu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga n’chifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:3 Nsanja ya Olonda,10/15/2012, tsa. 138/1/2000, tsa. 10
3 Choncho iwo anasonkhana n’kuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni, kuti: “Tatopa nanu tsopano! Khamu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga n’chifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?”+