Numeri 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi ukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti unatichotsa kudziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere m’chipululu muno,+ kutinso ukhale ngati mfumu yomatilamula?+
13 Kodi ukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti unatichotsa kudziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere m’chipululu muno,+ kutinso ukhale ngati mfumu yomatilamula?+