Numeri 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mose atamva zimenezi anakwiya kwambiri, ndipo anauza Yehova kuti: “Nsembe zawo zambewu musaziyang’ane.+ Ine sindinawalande ngakhale bulu mmodzi wamphongo, kapena kuchitira choipa aliyense wa iwo.”+
15 Mose atamva zimenezi anakwiya kwambiri, ndipo anauza Yehova kuti: “Nsembe zawo zambewu musaziyang’ane.+ Ine sindinawalande ngakhale bulu mmodzi wamphongo, kapena kuchitira choipa aliyense wa iwo.”+