Numeri 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nthawi yomweyo anthuwo anachoka kumbali zonse za mahema a Kora, Datani ndi Abiramu. Zitatero, Datani ndi Abiramu anatuluka n’kuima pamakomo a mahema awo,+ limodzi ndi akazi awo, ana awo.
27 Nthawi yomweyo anthuwo anachoka kumbali zonse za mahema a Kora, Datani ndi Abiramu. Zitatero, Datani ndi Abiramu anatuluka n’kuima pamakomo a mahema awo,+ limodzi ndi akazi awo, ana awo.