-
Numeri 16:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Nthawi yomweyo Aroni anatenga chofukiziracho monga anamuuzira Mose, n’kuthamanga kukalowa pakati pa mpingowo. Koma mliri unali utayamba kale pakati pawo. Choncho Aroni anaika nsembe ija pamoto n’kuyamba kuwaphimbira machimo anthuwo.
-