Numeri 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azikhala pafupi nanu kuti azichita utumiki wawo wonse wa pachihema chokumanako, ndipo munthu wina aliyense amene si Mlevi asayandikire kwa inu.+
4 Azikhala pafupi nanu kuti azichita utumiki wawo wonse wa pachihema chokumanako, ndipo munthu wina aliyense amene si Mlevi asayandikire kwa inu.+