Numeri 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Isiraeli asadzayandikirenso chihema chokumanako, kuti angadzachimwe n’kufa.+