-
Numeri 19:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Akatha, wansembeyo achape zovala zake n’kusamba thupi lake ndi madzi. Pambuyo pake akhoza kulowa mumsasa, koma akhalebe wodetsedwa mpaka madzulo.
-