-
Numeri 19:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Munthu wodetsedwayo am’tapireko phulusa la nsembe yamachimo yotenthedwa ija. Phulusalo aliike m’mbiya n’kuthiramo madzi a kumtsinje.
-