Numeri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anthuwo anayamba kukangana+ ndi Mose, kuti: “Zikanakhala bwino tikanangofera limodzi ndi abale athu amene anafa pamaso pa Yehova aja.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2019, ptsa. 12-13
3 Pamenepo anthuwo anayamba kukangana+ ndi Mose, kuti: “Zikanakhala bwino tikanangofera limodzi ndi abale athu amene anafa pamaso pa Yehova aja.+