Numeri 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsiku lina Mose anatumiza amithenga kuchokera ku Kadesi kumene iwo anali, kupita kwa mfumu ya Edomu,+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene ationekera ife.+
14 Tsiku lina Mose anatumiza amithenga kuchokera ku Kadesi kumene iwo anali, kupita kwa mfumu ya Edomu,+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene ationekera ife.+