Numeri 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma iye anakanabe, kuti: “Ayi, musadzere+ m’dziko langa.” Mfumu ya Edomu+ itanena zimenezi, inatuluka ndi chikhamu cha anthu, ndi gulu la asilikali lamphamvu, kuti akawathire nkhondo.
20 Koma iye anakanabe, kuti: “Ayi, musadzere+ m’dziko langa.” Mfumu ya Edomu+ itanena zimenezi, inatuluka ndi chikhamu cha anthu, ndi gulu la asilikali lamphamvu, kuti akawathire nkhondo.