Numeri 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Aroni aikidwe m’manda, agone ndi makolo ake,+ pakuti sadzalowa m’dziko limene ndidzapatse ana a Isiraeli. Izi zili choncho chifukwa amuna inu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 14-15 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 19
24 “Aroni aikidwe m’manda, agone ndi makolo ake,+ pakuti sadzalowa m’dziko limene ndidzapatse ana a Isiraeli. Izi zili choncho chifukwa amuna inu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+