Numeri 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe n’kuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika m’phirimo.
28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe n’kuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika m’phirimo.