Numeri 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno buluyo anaona mngelo wa Yehova ali chilili pamsewu lupanga lake lili m’manja.+ Pamenepo buluyo anayesetsa kupatukira kumbali kwa msewu kuti adutse kutchire, koma Balamu anayamba kum’kwapula kuti am’bwezere mumsewu.
23 Ndiyeno buluyo anaona mngelo wa Yehova ali chilili pamsewu lupanga lake lili m’manja.+ Pamenepo buluyo anayesetsa kupatukira kumbali kwa msewu kuti adutse kutchire, koma Balamu anayamba kum’kwapula kuti am’bwezere mumsewu.