Numeri 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mulungu atam’peza Balamu,+ iye anamuuza Mulunguyo kuti: “Ndamanga maguwa ansembe 7 m’mizere, ndipo ndapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.”+
4 Mulungu atam’peza Balamu,+ iye anamuuza Mulunguyo kuti: “Ndamanga maguwa ansembe 7 m’mizere, ndipo ndapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.”+