-
Numeri 23:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Iye atabwerera kwa Balaki, anapeza Balakiyo limodzi ndi akalonga onse a ku Mowabu ataima pafupi ndi nsembe yake yopsereza.
-