Numeri 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndani watha kuwerenga mtundu wa Yakobo,+ wochuluka ngati fumbi,Ndipo ndani watha kuwerenga gawo limodzi mwa magawo anayi a Isiraeli?Moyo wanga ufe imfa ya olungama,+Ndipo mathero anga akhale ngati awo.”+
10 Ndani watha kuwerenga mtundu wa Yakobo,+ wochuluka ngati fumbi,Ndipo ndani watha kuwerenga gawo limodzi mwa magawo anayi a Isiraeli?Moyo wanga ufe imfa ya olungama,+Ndipo mathero anga akhale ngati awo.”+