Numeri 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye sanaone mphamvu yamatsenga+ iliyonse ikuchita kanthu pa Yakobo,Ndipo sanaone Isiraeli akuponyeredwa vuto.Mulungu wake Yehova ali naye,+Ndipo mfuu yotamanda mfumu ikumveka pakati pake.
21 Iye sanaone mphamvu yamatsenga+ iliyonse ikuchita kanthu pa Yakobo,Ndipo sanaone Isiraeli akuponyeredwa vuto.Mulungu wake Yehova ali naye,+Ndipo mfuu yotamanda mfumu ikumveka pakati pake.