Numeri 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumeneko Balamu+ anauza Balaki kuti: “Mundimangire pamalo ano maguwa ansembe 7, ndipo mundikonzere ng’ombe zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.”+
29 Kumeneko Balamu+ anauza Balaki kuti: “Mundimangire pamalo ano maguwa ansembe 7, ndipo mundikonzere ng’ombe zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.”+