Numeri 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 53, 318 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 17
17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo.