Numeri 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anapitiriza kulankhula mawu ake a ndakatulo, kuti:“Kalanga ine! Adzapulumuke tsokalo ndani, Mulungu akadzaliponya?+
23 Iye anapitiriza kulankhula mawu ake a ndakatulo, kuti:“Kalanga ine! Adzapulumuke tsokalo ndani, Mulungu akadzaliponya?+